-
Ekisodo 30:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Ulikute ndi golide woyenga bwino pamwamba pake ndi mʼmbali mwake kuzungulira guwalo komanso nyanga zake. Upange mkombero wagolide kuzungulira guwa lonselo.
-