2 “Tenga Aroni limodzi ndi ana ake,+ zovala zawo,+ mafuta odzozera,+ ngʼombe yamphongo ya nsembe yamachimo, nkhosa ziwiri zamphongo ndi dengu la mikate yopanda zofufumitsa.+
17“Musamapereke kwa Yehova Mulungu wanu nsembe ya ngʼombe kapena nkhosa imene ili ndi chilema kapena vuto lililonse, chifukwa idzakhala yonyansa kwa Yehova Mulungu wanu.+