Ekisodo 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Kenako udzoze Aroni+ ndi ana ake+ ndipo uwayeretse kuti atumikire monga ansembe anga.+ Aheberi 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mkulu wa ansembe aliyense wotengedwa pakati pa anthu, amaikidwa kuti azigwira ntchito ya Mulungu mʼmalo mwa anthu,+ kuti azipereka mphatso ndi nsembe zophimba machimo.+
5 Mkulu wa ansembe aliyense wotengedwa pakati pa anthu, amaikidwa kuti azigwira ntchito ya Mulungu mʼmalo mwa anthu,+ kuti azipereka mphatso ndi nsembe zophimba machimo.+