Aheberi 9:21, 22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo anawazanso magazi aja pachihema ndi ziwiya zonse zogwiritsa ntchito pa utumiki wopatulika.+ 22 Mogwirizana ndi Chilamulo, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ ndipo popanda kukhetsa magazi anthu sangakhululukidwe machimo awo.+
21 Ndipo anawazanso magazi aja pachihema ndi ziwiya zonse zogwiritsa ntchito pa utumiki wopatulika.+ 22 Mogwirizana ndi Chilamulo, pafupifupi zinthu zonse zimayeretsedwa ndi magazi+ ndipo popanda kukhetsa magazi anthu sangakhululukidwe machimo awo.+