Ekisodo 29:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ukatero utengeko magazi a ngʼombeyo ndi chala chako ndipo uwapake panyanga za guwa lansembe.+ Magazi otsalawo uwathire pansi pa guwa lansembe.+ Levitiko 8:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Mose anapha ngʼombeyo nʼkutenga magazi+ ndi chala chake ndipo anawapaka panyanga zonse za guwa lansembe nʼkuyeretsa guwalo ku uchimo. Koma magazi otsalawo anawathira pansi pa guwa lansembe kuti alipatule, kuphimba machimo paguwalo.
12 Ukatero utengeko magazi a ngʼombeyo ndi chala chako ndipo uwapake panyanga za guwa lansembe.+ Magazi otsalawo uwathire pansi pa guwa lansembe.+
15 Ndiyeno Mose anapha ngʼombeyo nʼkutenga magazi+ ndi chala chake ndipo anawapaka panyanga zonse za guwa lansembe nʼkuyeretsa guwalo ku uchimo. Koma magazi otsalawo anawathira pansi pa guwa lansembe kuti alipatule, kuphimba machimo paguwalo.