Ekisodo 25:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mupangenso akerubi awiri agolide. Akhale osula ndipo muwaike kumapeto onse awiri a chivundikirocho.+ Ekisodo 25:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chivundikirocho+ udzachiike pa Likasalo, ndipo mu Likasamo udzaikemo Umboni umene ndidzakupatse. 1 Mbiri 28:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Atatero, Davide anapatsa Solomo mwana wake mapulani akamangidwe+ ka khonde+ ndi nyumba zake, zipinda zake zosungiramo katundu, zipinda zake zapadenga, zipinda zake zamkati ndiponso nyumba yokhalamo chivundikiro chophimbira machimo.+
18 Mupangenso akerubi awiri agolide. Akhale osula ndipo muwaike kumapeto onse awiri a chivundikirocho.+
11 Atatero, Davide anapatsa Solomo mwana wake mapulani akamangidwe+ ka khonde+ ndi nyumba zake, zipinda zake zosungiramo katundu, zipinda zake zapadenga, zipinda zake zamkati ndiponso nyumba yokhalamo chivundikiro chophimbira machimo.+