Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 53:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa chifukwa chimenechi, ndidzamupatsa gawo pamodzi ndi ambiri,

      Ndipo iye adzagawana ndi amphamvu katundu amene alanda kunkhondo,

      Chifukwa anapereka moyo wake*+

      Ndipo anaikidwa mʼgulu la anthu ochimwa.+

      Ananyamula tchimo la anthu ambiri+

      Ndipo analowererapo kuti athandize anthu ochimwa.+

  • Aefeso 1:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Kudzera mwa mwana wakeyu, tinamasulidwa ndi dipo* la magazi ake,+ inde, takhululukidwa machimo athu,+ mogwirizana ndi kukoma mtima kwake kwakukulu.

  • Aheberi 9:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 nayenso Khristu anaperekedwa nsembe kamodzi kokha kuti anyamule machimo a anthu ambiri.+ Nthawi yachiwiri imene adzaonekere sadzaonekera nʼcholinga chochotsa uchimo. Ndipo amene adzamuone ndi anthu amene akumuyembekezera ndi mtima wonse kuti awapulumutse.+

  • 1 Petulo 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Iye ananyamula machimo athu+ mʼthupi lake pamene anamukhomerera pamtengo.+ Anachita zimenezi kuti tipulumutsidwe ku uchimo nʼkumachita zinthu zolungama. Ndipo “munachiritsidwa ndi mabala ake.”+

  • 1 Yohane 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Inu mukudziwanso kuti iye anaonekera kuti achotse machimo athu+ ndipo mwa iye mulibe tchimo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena