Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 16:21, 22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndipo Aroni aziika manja ake onse pamutu pa mbuziyo ndi kuvomereza zolakwa zonse za Aisiraeli ndiponso machimo awo onse. Zonsezi aziziika pamutu pa mbuzi+ ija nʼkuipereka kwa munthu amene amusankhiratu kuti akaisiye kuchipululu. 22 Mbuziyo izinyamula zolakwa zawo zonse+ pamutu pake ndipo aziitumiza kuchipululu.+

  • Yesaya 53:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Chifukwa cha kuvutika kwake, iye adzaona zabwino ndipo adzakhutira.

      Chifukwa cha zimene mtumiki wanga wolungama akudziwa,+

      Adzachititsa kuti anthu ambiri azionedwa olungama,+

      Ndipo adzanyamula zolakwa zawo.+

  • Yohane 1:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Tsiku lotsatira anaona Yesu akubwera kwa iye, ndipo anati: “Taonani, Mwanawankhosa+ wa Mulungu amene akuchotsa uchimo+ wa dziko!+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena