Levitiko 16:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma mbuzi imene maere asonyeza kuti ndi yotenga machimo a anthu, aziibweretsa yamoyo nʼkuiimika pamaso pa Yehova kuti machimo a anthu aphimbidwe. Akatero aziitumiza mʼchipululu monga mbuzi yotenga machimo a anthu.+ Salimo 103:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mofanana ndi mmene kotulukira dzuwa kwatalikirana ndi kolowera dzuwa,Mulungu waikanso zolakwa zathu kutali ndi ife.+ Aheberi 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho nayenso Yesu anakavutikira kunja kwa geti la mzinda+ kuti ayeretse anthu ndi magazi ake.+
10 Koma mbuzi imene maere asonyeza kuti ndi yotenga machimo a anthu, aziibweretsa yamoyo nʼkuiimika pamaso pa Yehova kuti machimo a anthu aphimbidwe. Akatero aziitumiza mʼchipululu monga mbuzi yotenga machimo a anthu.+
12 Mofanana ndi mmene kotulukira dzuwa kwatalikirana ndi kolowera dzuwa,Mulungu waikanso zolakwa zathu kutali ndi ife.+