Levitiko 16:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Aroni azichita maere pa mbuzi ziwirizo. Maere amodzi akhale a Yehova, ndipo ena akhale a mbuzi yotenga machimo a anthu.* Levitiko 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo Aroni aziika manja ake onse pamutu pa mbuziyo ndi kuvomereza zolakwa zonse za Aisiraeli ndiponso machimo awo onse. Zonsezi aziziika pamutu pa mbuzi+ ija nʼkuipereka kwa munthu amene amusankhiratu kuti akaisiye kuchipululu.
8 Ndiyeno Aroni azichita maere pa mbuzi ziwirizo. Maere amodzi akhale a Yehova, ndipo ena akhale a mbuzi yotenga machimo a anthu.*
21 Ndipo Aroni aziika manja ake onse pamutu pa mbuziyo ndi kuvomereza zolakwa zonse za Aisiraeli ndiponso machimo awo onse. Zonsezi aziziika pamutu pa mbuzi+ ija nʼkuipereka kwa munthu amene amusankhiratu kuti akaisiye kuchipululu.