Ekisodo 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Dziwani kuti Yehova wakupatsani Sabata.+ Nʼchifukwa chake pa tsiku la 6 akukupatsani chakudya cha masiku awiri. Pa tsiku la 7 aliyense azikhala pamalo ake. Munthu asachoke pamalo ake.” Ekisodo 20:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma tsiku la 7 ndi sabata la Yehova Mulungu wanu. Musamagwire ntchito iliyonse inuyo kapena mwana wanu wamwamuna, mwana wanu wamkazi, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, chiweto chanu kapena mlendo amene akukhala mumzinda wanu.*+ Ezekieli 20:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndinawapatsanso sabata langa+ kuti likhale chizindikiro pakati pa ine ndi iwowo.+ Ndinachita zimenezi nʼcholinga choti adziwe kuti ine Yehova, ndi amene ndikuwachititsa kuti akhale opatulika.
29 Dziwani kuti Yehova wakupatsani Sabata.+ Nʼchifukwa chake pa tsiku la 6 akukupatsani chakudya cha masiku awiri. Pa tsiku la 7 aliyense azikhala pamalo ake. Munthu asachoke pamalo ake.”
10 Koma tsiku la 7 ndi sabata la Yehova Mulungu wanu. Musamagwire ntchito iliyonse inuyo kapena mwana wanu wamwamuna, mwana wanu wamkazi, kapolo wanu wamwamuna, kapolo wanu wamkazi, chiweto chanu kapena mlendo amene akukhala mumzinda wanu.*+
12 Ndinawapatsanso sabata langa+ kuti likhale chizindikiro pakati pa ine ndi iwowo.+ Ndinachita zimenezi nʼcholinga choti adziwe kuti ine Yehova, ndi amene ndikuwachititsa kuti akhale opatulika.