Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 95:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Choncho ndinalumbira nditakwiya kuti:

      “Sadzalowa mumpumulo wanga.”+

  • Ezekieli 20:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndinalumbiranso kwa iwo mʼchipululu kuti sindidzawalowetsa mʼdziko limene ndinawapatsa,+ dziko loyenda mkaka ndi uchi+ komanso lokongola kwambiri kuposa mayiko onse.

  • Aheberi 3:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nanga kodi analumbirira ndani kuti sadzalowa mumpumulo wake? Kodi si omwe aja amene sanamumvere?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena