Numeri 14:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Nonsenu simudzalowa mʼdziko limene ndinalumbira* kuti mudzakhalamo,+ kupatula Kalebe mwana wa Yefune ndi Yoswa mwana wa Nuni.+ Salimo 95:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Choncho ndinalumbira nditakwiya kuti: “Sadzalowa mumpumulo wanga.”+ Salimo 106:26, 27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho Mulungu anawalumbirira atakweza dzanja lake,Kuti adzachititsa kuti afere mʼchipululu.+27 Adzachititsa kuti mbadwa zawo ziphedwe ndi anthu a mitundu ina,Ndiponso kuwamwaza mʼmayiko osiyanasiyana.+
30 Nonsenu simudzalowa mʼdziko limene ndinalumbira* kuti mudzakhalamo,+ kupatula Kalebe mwana wa Yefune ndi Yoswa mwana wa Nuni.+
26 Choncho Mulungu anawalumbirira atakweza dzanja lake,Kuti adzachititsa kuti afere mʼchipululu.+27 Adzachititsa kuti mbadwa zawo ziphedwe ndi anthu a mitundu ina,Ndiponso kuwamwaza mʼmayiko osiyanasiyana.+