Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 26:55
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 55 Koma dzikolo uligawe pochita maere.+ Onse alandire cholowa chawo potengera mayina a mafuko a makolo awo.

  • Numeri 33:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Mukagwiritse ntchito maere+ pogawa dzikolo kwa mabanja anu kuti likhale cholowa chanu. Banja la anthu ambiri mukaliwonjezere cholowa chawo, ndipo banja la anthu ochepa mukalichepetsere cholowa chawo.+ Banja lililonse mukalipatse cholowa mogwirizana ndi kumene maere a banjalo agwera. Mukalandira malo kuti akhale cholowa chanu potsata mafuko a makolo anu.+

  • Yoswa 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pogawa cholowacho kwa mafuko 9 ndi hafu,+ anachita maere+ mogwirizana ndi zimene Yehova analamula kudzera mwa Mose.

  • Yoswa 18:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Koma inuyo mukagawe dzikolo mʼzigawo 7 ndipo mukazilembe. Kenako mukabwere nazo kuno kuti ndidzakuchitireni maere+ pamaso pa Yehova Mulungu wathu.

  • Miyambo 16:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Maere amaponyedwa pachovala,+

      Koma zonse zimene maerewo asonyeza zimachokera kwa Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena