Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 32:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Choncho Mose anapereka malo kwa ana a Gadi, ana a Rubeni+ komanso hafu ya fuko la Manase+ mwana wa Yosefe. Anawapatsa malo a ufumu wa Sihoni+ mfumu ya Aamori, malo a ufumu wa Ogi+ mfumu ya Basana ndi dera lonse la mizinda komanso midzi yozungulira.

  • Deuteronomo 3:12, 13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pa nthawi imeneyo tinatenga dzikoli kukhala lathu kuchokera ku Aroweli,+ mzinda umene uli mʼchigwa cha Arinoni* ndi hafu ya dera lamapiri la Giliyadi. Ndipo ndinapereka mizinda yake kwa fuko la Rubeni ndi fuko la Gadi.+ 13 Mbali yotsala ya dera la Giliyadi ndi Basana yense amene anali mu ufumu wa Ogi ndinaipereka kwa hafu ya fuko la Manase.+ Dera lonse la Arigobi, limene ndi mbali ya Basana linkadziwika kuti ndi dziko la Arefai.

  • Yoswa 13:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Mose mtumiki wa Yehova anapereka cholowa kwa hafu ina ya fuko la Manase, kwa fuko la Rubeni ndi kwa fuko la Gadi, kutsidya lakumʼmawa kwa mtsinje wa Yorodano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena