Ekisodo 27:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Pakhomo la bwalolo pakhale nsalu yowomba yokwana mamita 9 mulitali mwake. Ikhale ya ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+ Pakhale zipilala 4 ndi zitsulo 4 zokhazikapo zipilalazo.+
16 Pakhomo la bwalolo pakhale nsalu yowomba yokwana mamita 9 mulitali mwake. Ikhale ya ulusi wabuluu, ubweya wa nkhosa wapepo, ulusi wofiira kwambiri ndi ulusi wopota wabwino kwambiri.+ Pakhale zipilala 4 ndi zitsulo 4 zokhazikapo zipilalazo.+