Numeri 4:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Utumiki umene mabanja a ana a Gerisoni azichita mʼchihema chokumanako+ ndi umenewu. Itamara+ mwana wa wansembe Aroni, ndi amene aziyangʼanira utumiki wawo.
28 Utumiki umene mabanja a ana a Gerisoni azichita mʼchihema chokumanako+ ndi umenewu. Itamara+ mwana wa wansembe Aroni, ndi amene aziyangʼanira utumiki wawo.