Levitiko 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako wansembe azitengako pangʼono nsembe yambewu kuimira nsembe yonseyo,+ ndipo aziwotcha zimene watengazo paguwa lansembe. Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa* yoperekedwa kwa Yehova.+
9 Kenako wansembe azitengako pangʼono nsembe yambewu kuimira nsembe yonseyo,+ ndipo aziwotcha zimene watengazo paguwa lansembe. Imeneyi ndi nsembe yowotcha pamoto yakafungo kosangalatsa* yoperekedwa kwa Yehova.+