Numeri 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Manase.+ Mtsogoleri wa ana a Manase ndi Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri. Numeri 10:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mtsogoleri wa gulu la fuko la ana a Manase anali Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri.
20 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Manase.+ Mtsogoleri wa ana a Manase ndi Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri.