Numeri 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano atsogoleriwo anapereka zopereka zawo pamwambo wotsegulira+ guwa lansembe, pa tsiku limene guwalo linadzozedwa. Atsogoleriwo atabweretsa zopereka zawozo paguwa lansembe, Ezara 2:68 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 68 Atsogoleri ena a nyumba za makolo awo atafika kunyumba ya Yehova imene inali ku Yerusalemu, anapereka zopereka zaufulu+ kunyumba ya Mulungu woona kuti imangidwenso pamalo ake.+
10 Tsopano atsogoleriwo anapereka zopereka zawo pamwambo wotsegulira+ guwa lansembe, pa tsiku limene guwalo linadzozedwa. Atsogoleriwo atabweretsa zopereka zawozo paguwa lansembe,
68 Atsogoleri ena a nyumba za makolo awo atafika kunyumba ya Yehova imene inali ku Yerusalemu, anapereka zopereka zaufulu+ kunyumba ya Mulungu woona kuti imangidwenso pamalo ake.+