Numeri 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano atsogoleriwo anapereka zopereka zawo pamwambo wotsegulira+ guwa lansembe, pa tsiku limene guwalo linadzozedwa. Atsogoleriwo atabweretsa zopereka zawozo paguwa lansembe,
10 Tsopano atsogoleriwo anapereka zopereka zawo pamwambo wotsegulira+ guwa lansembe, pa tsiku limene guwalo linadzozedwa. Atsogoleriwo atabweretsa zopereka zawozo paguwa lansembe,