Ekisodo 40:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Mʼzigawo zonse za ulendo wawo, mtambowo ukachoka pamwamba pa chihemacho nʼkukwera mʼmwamba, Aisiraeli ankanyamuka nʼkuyamba ulendo.+ Salimo 78:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Iye ankawatsogolera ndi mtambo masanaNdipo usiku wonse ankawatsogolera ndi kuwala kwa moto.+
36 Mʼzigawo zonse za ulendo wawo, mtambowo ukachoka pamwamba pa chihemacho nʼkukwera mʼmwamba, Aisiraeli ankanyamuka nʼkuyamba ulendo.+