Levitiko 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Lankhula ndi Aisiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Mʼmwezi wa 7, pa tsiku loyamba la mweziwo, muzipuma pa ntchito zanu zonse. Limeneli ndi tsiku la chikumbutso, ndipo lipenga likalira+ muzisonkhana kuti mulambire Mulungu. Numeri 29:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 “‘Pa tsiku loyamba la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa.+ Tsiku limeneli lizikhala tsiku loliza lipenga.+
24 “Lankhula ndi Aisiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Mʼmwezi wa 7, pa tsiku loyamba la mweziwo, muzipuma pa ntchito zanu zonse. Limeneli ndi tsiku la chikumbutso, ndipo lipenga likalira+ muzisonkhana kuti mulambire Mulungu.
29 “‘Pa tsiku loyamba la mwezi wa 7, muzichita msonkhano wopatulika. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa.+ Tsiku limeneli lizikhala tsiku loliza lipenga.+