Numeri 32:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yehova anawakwiyira koopsa Aisiraeli ndipo anawachititsa kuti azingoyendayenda mʼchipululu kwa zaka 40,+ mpaka mʼbadwo wonse wochita zoipa pamaso pa Yehova utatha.+ Yoswa 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yehova wandisunga ndi moyo+ mogwirizana ndi zimene analonjeza.+ Tsopano padutsa zaka 45 kuchokera pamene Yehova analonjeza Mose pa nthawi imene Aisiraeli anali mʼchipululu.+ Lero ndili ndi zaka 85.
13 Yehova anawakwiyira koopsa Aisiraeli ndipo anawachititsa kuti azingoyendayenda mʼchipululu kwa zaka 40,+ mpaka mʼbadwo wonse wochita zoipa pamaso pa Yehova utatha.+
10 Yehova wandisunga ndi moyo+ mogwirizana ndi zimene analonjeza.+ Tsopano padutsa zaka 45 kuchokera pamene Yehova analonjeza Mose pa nthawi imene Aisiraeli anali mʼchipululu.+ Lero ndili ndi zaka 85.