Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 29:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Kenako utenge chidale cha nkhosa yoikira+ Aroni kuti akhale wansembe ndipo uchiyendetse uku ndi uku monga nsembe yoperekedwa kwa Yehova. Imeneyo idzakhale yako.

  • Levitiko 7:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Wansembe aziwotcha mafutawo paguwa lansembe,+ koma chidalecho chizikhala cha Aroni ndi ana ake.+

  • Levitiko 7:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ine ndikutenga chidale cha nsembe yoyendetsa uku ndi uku ndiponso mwendo womwe ndi gawo lopatulika. Ndikutenga zimenezi pansembe zamgwirizano za Aisiraeli nʼkuzipereka kwa Aroni wansembe ndi ana ake. Limeneli ndi lamulo kwa Aisiraeli mpaka kalekale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena