Numeri 22:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Mʼmawa kutacha, Balaki anakatenga Balamu nʼkupita naye ku Bamoti-baala. Anapita naye kumeneko kuti akathe kuliona bwino gulu lonse la Aisiraeli.+ Numeri 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Balamu anauza Balaki kuti: “Mumange maguwa ansembe okwanira 7+ pamalo ano. Mukatero mundikonzere ngʼombe zamphongo 7 ndi nkhosa zamphongo 7.” Numeri 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Choncho anamutengera ku Zofimu, pamwamba pa phiri la Pisiga.+ Kumeneko anamanga maguwa ansembe 7, nʼkupereka nsembe ngʼombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+
41 Mʼmawa kutacha, Balaki anakatenga Balamu nʼkupita naye ku Bamoti-baala. Anapita naye kumeneko kuti akathe kuliona bwino gulu lonse la Aisiraeli.+
23 Kenako Balamu anauza Balaki kuti: “Mumange maguwa ansembe okwanira 7+ pamalo ano. Mukatero mundikonzere ngʼombe zamphongo 7 ndi nkhosa zamphongo 7.”
14 Choncho anamutengera ku Zofimu, pamwamba pa phiri la Pisiga.+ Kumeneko anamanga maguwa ansembe 7, nʼkupereka nsembe ngʼombe yamphongo ndi nkhosa yamphongo paguwa lililonse.+