Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 31:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Pajatu akazi amenewa ndi amene anatsatira mawu a Balamu nʼkunyengerera Aisiraeli kuti achimwire Yehova+ pa zimene zinachitika ku Peori,+ moti mliri unagwera gulu la anthu a Yehova.+

  • 1 Akorinto 10:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Komanso tisamachite chiwerewere,* mmene ena a iwo anachitira, nʼkufa anthu 23,000 tsiku limodzi.+

  • Chivumbulutso 2:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ngakhale zili choncho, ndakupeza ndi milandu ingapo. Iwe kumeneko uli ndi anthu amene akupitiriza kutsatira chiphunzitso cha Balamu,+ amene anaphunzitsa Balaki+ kuti aikire ana a Isiraeli chopunthwitsa kuti adye zoperekedwa nsembe kwa mafano ndi kuchita chiwerewere.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena