23 Anthu a mitundu ina adzadziwa kuti a nyumba ya Isiraeli anatengedwa kupita ku ukapolo chifukwa cha zolakwa zawo, popeza anandichitira zinthu mosakhulupirika.+ Choncho ine ndinawabisira nkhope yanga+ nʼkuwapereka kwa adani awo+ ndipo onse anaphedwa ndi lupanga.