1 Mbiri 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola, ulemerero ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi zapadziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu ndi wanu, inu Yehova.+ Ndinu Wokwezeka ndiponso ndinu mutu pa onse. Salimo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dziko lapansi ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka komanso onse okhala panthakapo ndi ake. Salimo 115:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Kunena za kumwamba, kumwamba ndi kwa Yehova,+Koma dziko lapansi analipereka kwa ana a anthu.+
11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola, ulemerero ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi zapadziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu ndi wanu, inu Yehova.+ Ndinu Wokwezeka ndiponso ndinu mutu pa onse.
24 Dziko lapansi ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka komanso onse okhala panthakapo ndi ake.