-
Yoswa 5:1Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 Mafumu onse a Aamori+ amene anali kutsidya la kumadzulo kwa mtsinje wa Yorodano, ndi mafumu onse a Akanani+ amene anali mʼmbali mwa nyanja, anamva kuti Yehova anaphwetsa madzi a mtsinje wa Yorodano mpaka Aisiraeli onse atawoloka. Atangomva zimenezo, anachita mantha kwambiri,*+ moti analibenso mphamvu chifukwa choopa Aisiraeli.+
-