-
Ezara 9:7Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
7 Kuyambira masiku a makolo athu mpaka lero machimo athu achuluka.+ Chifukwa cha zolakwa zathu, ifeyo, mafumu athu ndi ansembe athu, taperekedwa mʼmanja mwa mafumu a mayiko ena, taphedwa ndi lupanga,+ tatengedwa kupita ku ukapolo,+ talandidwa katundu+ komanso takhala amanyazi ngati mmene tilili lero.+
-