Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 32:40, 41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Choncho Mose anapereka mzinda wa Giliyadi kwa Makiri mwana wa Manase, ndipo iye anayamba kukhala mmenemo.+ 41 Yairi mwana wa Manase anaukira Aamori nʼkulanda midzi yawo ingʼonoingʼono. Midzi imeneyi anayamba kuitchula kuti Havoti-yairi.*+

  • Deuteronomo 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Yairi+ mwana wamwamuna wa Manase anatenga dera lonse la Arigobi+ mpaka kumalire a Agesuri ndi a Amaakati.+ Midzi ya ku Basana imeneyo anaipatsa dzina lofanana ndi lake lakuti, Havoti-yairi*+ ndipo imadziwika ndi dzina limeneli mpaka pano.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena