Numeri 33:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Mukathamangitse anthu onse amene akukhala mʼdzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala+ ndi mafano awo onse achitsulo*+ komanso mukagwetse malo awo onse opatulika.+ Numeri 33:55 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 55 Koma ngati simukathamangitsa anthu amene akukhala mʼdzikolo,+ anthu amene mukawasiyewo adzakhala ngati zitsotso mʼmaso mwanu, ndiponso ngati minga yokubayani mʼnthiti mwanu. Ndipo iwo azidzakuvutitsani mʼdziko limene muzidzakhala.+
52 Mukathamangitse anthu onse amene akukhala mʼdzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala+ ndi mafano awo onse achitsulo*+ komanso mukagwetse malo awo onse opatulika.+
55 Koma ngati simukathamangitsa anthu amene akukhala mʼdzikolo,+ anthu amene mukawasiyewo adzakhala ngati zitsotso mʼmaso mwanu, ndiponso ngati minga yokubayani mʼnthiti mwanu. Ndipo iwo azidzakuvutitsani mʼdziko limene muzidzakhala.+