-
Salimo 83:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Anthu awo olemekezeka muwachititse kukhala ngati Orebi ndi Zeebi.+
Ndipo akalonga* awo muwachititse kukhala ngati Zeba ndi Zalimuna.+
-