Oweruza 6:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako, kunabwera mngelo wa Yehova+ nʼkukhala pansi pa mtengo waukulu ku Ofira. Mtengo umenewu unali wa Yowasi, Mwabi-ezeri.+ Pa nthawiyi, Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, ankapuntha tirigu moponderamo mphesa kuti Amidiyani asaone. Oweruza 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Gidiyoni anatenga golideyo nʼkupanga chovala cha efodi,+ ndipo anachiika pamalo oonekera mumzinda wakwawo wa Ofira.+ Aisiraeli onse anayamba kuchilambira,*+ moti chinakhala msampha kwa Gidiyoni ndi anthu a mʼbanja lake.+
11 Kenako, kunabwera mngelo wa Yehova+ nʼkukhala pansi pa mtengo waukulu ku Ofira. Mtengo umenewu unali wa Yowasi, Mwabi-ezeri.+ Pa nthawiyi, Gidiyoni+ mwana wa Yowasi, ankapuntha tirigu moponderamo mphesa kuti Amidiyani asaone.
27 Gidiyoni anatenga golideyo nʼkupanga chovala cha efodi,+ ndipo anachiika pamalo oonekera mumzinda wakwawo wa Ofira.+ Aisiraeli onse anayamba kuchilambira,*+ moti chinakhala msampha kwa Gidiyoni ndi anthu a mʼbanja lake.+