Genesis 9:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+ Oweruza 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Atatero anapita kunyumba kwa bambo ake ku Ofira+ nʼkupha abale ake,+ ana aamuna 70 a Yerubaala, ndipo anawaphera pamwala umodzi. Amene anapulumuka anali Yotamu yekha, mwana wamngʼono mwa ana aamuna a Yerubaala, chifukwa anabisala.
6 Aliyense wopha munthu, nayenso adzaphedwa ndi munthu,*+ chifukwa Mulungu anapanga munthu mʼchifaniziro chake.+
5 Atatero anapita kunyumba kwa bambo ake ku Ofira+ nʼkupha abale ake,+ ana aamuna 70 a Yerubaala, ndipo anawaphera pamwala umodzi. Amene anapulumuka anali Yotamu yekha, mwana wamngʼono mwa ana aamuna a Yerubaala, chifukwa anabisala.