2 Samueli 23:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Awa ndi mayina a asilikali amphamvu a Davide:+ Yosebu-basebete mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 800 nthawi imodzi. 1 Mbiri 19:8, 9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Davide atamva zimenezi, anatumiza Yowabu+ ndi gulu lonse lankhondo, limodzinso ndi asilikali ake amphamvu.+ 9 Ndiyeno Aamoni anapita kukaima pageti la mzinda atakonzekera kumenya nkhondo. Pomwe mafumu omwe anabwera aja anali kwaokha kutchire.
8 Awa ndi mayina a asilikali amphamvu a Davide:+ Yosebu-basebete mbadwa ya Hakemoni, mtsogoleri wa amuna atatu.+ Iye anatenga mkondo wake nʼkupha anthu 800 nthawi imodzi.
8 Davide atamva zimenezi, anatumiza Yowabu+ ndi gulu lonse lankhondo, limodzinso ndi asilikali ake amphamvu.+ 9 Ndiyeno Aamoni anapita kukaima pageti la mzinda atakonzekera kumenya nkhondo. Pomwe mafumu omwe anabwera aja anali kwaokha kutchire.