Salimo 148:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Anthu komanso zolengedwa zina zonse, atamande dzina la Yehova,Chifukwa dzina lake lokhalo lili pamwamba poti aliyense sangafikepo.+ Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+ Yeremiya 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Kodi pali munthu amene angabisale pamalo obisika amene ine sindingamuone?”+ akutero Yehova. “Kodi kumwamba kapena padziko lapansi, pali chilichonse chimene sindingachione?”+ akutero Yehova.
13 Anthu komanso zolengedwa zina zonse, atamande dzina la Yehova,Chifukwa dzina lake lokhalo lili pamwamba poti aliyense sangafikepo.+ Ulemerero wake uli pamwamba kuposa dziko lapansi ndi kumwamba.+
24 “Kodi pali munthu amene angabisale pamalo obisika amene ine sindingamuone?”+ akutero Yehova. “Kodi kumwamba kapena padziko lapansi, pali chilichonse chimene sindingachione?”+ akutero Yehova.