Nehemiya 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pa tsiku limenelo buku la Mose linawerengedwa anthu onse akumva.+ Iwo anapeza kuti mʼbukumo analembamo kuti mbadwa iliyonse ya Amoni ndi ya Mowabu+ isamaloledwe kukhala mʼgulu la anthu a Mulungu woona,+ Nehemiya 13:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho atangomva Chilamulocho, anayamba kuchotsa anthu a mitundu ina pakati pa Aisiraeli.+
13 Pa tsiku limenelo buku la Mose linawerengedwa anthu onse akumva.+ Iwo anapeza kuti mʼbukumo analembamo kuti mbadwa iliyonse ya Amoni ndi ya Mowabu+ isamaloledwe kukhala mʼgulu la anthu a Mulungu woona,+