-
Ezara 10:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Kenako wansembe Ezara anaimirira nʼkuuza anthuwo kuti: “Inu mwachita zosakhulupirika chifukwa mwatenga akazi achilendo+ ndipo mwawonjezera machimo a Isiraeli. 11 Choncho vomerezani machimo anu kwa Yehova Mulungu wa makolo anu ndipo chitani zomusangalatsa. Musiyane ndi anthu a mitundu ina ndiponso akazi achilendowa.”+
-