-
1 Mbiri 9:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Panalinso Bakabakara, Heresi, Galali ndi Mataniya mwana wa Mika. Mika anali mwana wa Zikiri ndipo Zikiri anali mwana wa Asafu.
-
-
Nehemiya 11:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Komanso panali Mataniya+ mwana wa Mika ndipo Mika anali mwana wa Zabidi. Zabidi anali mwana wa Asafu,+ yemwe anali mtsogoleri wa nyimbo zotamanda Mulungu. Iye ankatsogolera potamanda Mulungu pa nthawi ya pemphero.+ Bakibukiya anali wachiwiri wake poyangʼanira abale ake. Panalinso Abada mwana wa Samuwa, Samuwa anali mwana wa Galali ndipo Galali anali mwana wa Yedutuni.+
-