Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 2:54
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 54 Ana a Salima anali anthu okhala ku Betelehemu,+ ku Netofa ndi ku Atiroti-beti-yowabu. Hafu ya anthu a ku Manahati ndi anthu a ku Zora, analinso ana a Salima.

  • 1 Mbiri 9:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Oyamba kubwerera nʼkukakhala kucholowa chawo mʼmizinda yawo anali Aisiraeli ena, ansembe, Alevi ndi atumiki apakachisi.*+

  • 1 Mbiri 9:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Komanso panali Obadiya mwana wa Semaya. Semaya anali mwana wa Galali, Galali anali mwana wa Yedutuni. Ndiye panalinso Berekiya mwana wa Asa mwana wa Elikana, amene ankakhala mʼmidzi ya Anetofa.+

  • Nehemiya 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Awa ndi anthu amʼchigawo amene anachoka ku ukapolo, anthu omwe Nebukadinezara+ mfumu ya ku Babulo anawatenga nʼkupita nawo ku ukapolo.+ Anthuwa anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense mumzinda wakwawo.+

  • Nehemiya 7:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Amuna a ku Betelehemu ndi ku Netofa, 188.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena