Esitere 8:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kuwonjezera pamenepo, Esitere analankhulanso ndi mfumu. Iye anagwada pamapazi a mfumuyo ndipo anachonderera kuti mfumu isinthe chiwembu chimene Hamani, mbadwa ya Agagi, anakonzera Ayuda.+
3 Kuwonjezera pamenepo, Esitere analankhulanso ndi mfumu. Iye anagwada pamapazi a mfumuyo ndipo anachonderera kuti mfumu isinthe chiwembu chimene Hamani, mbadwa ya Agagi, anakonzera Ayuda.+