Yobu 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Zimenezi ndi zimene zidzachitikire* anthu onse amene aiwala Mulungu,Chifukwa chiyembekezo cha anthu oipa* chidzatha, Yobu 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umu ndi mmene adzathere,*+Kenako zomera zina zidzamera kuchokera mufumbi. Yobu 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa mukunena kuti, ‘Kodi nyumba ya munthu wolemekezeka ili kuti,Nanga tenti imene munthu woipa ankakhala ili kuti?’+
13 Zimenezi ndi zimene zidzachitikire* anthu onse amene aiwala Mulungu,Chifukwa chiyembekezo cha anthu oipa* chidzatha, Yobu 8:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umu ndi mmene adzathere,*+Kenako zomera zina zidzamera kuchokera mufumbi. Yobu 21:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Chifukwa mukunena kuti, ‘Kodi nyumba ya munthu wolemekezeka ili kuti,Nanga tenti imene munthu woipa ankakhala ili kuti?’+
28 Chifukwa mukunena kuti, ‘Kodi nyumba ya munthu wolemekezeka ili kuti,Nanga tenti imene munthu woipa ankakhala ili kuti?’+