Deuteronomo 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Taonani, kumwamba ndi kwa Yehova Mulungu wanu, ngakhale kumwamba kwa kumwambako* komanso dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo zonsezo ndi zake.+ Salimo 24:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Dziko lapansi ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka komanso onse okhala panthakapo ndi ake. Salimo 50:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ngakhale nditakhala ndi njala, sindingakuuzeni,Chifukwa dziko lonse ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndi zanga.+ 1 Akorinto 10:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Chifukwa “dziko lapansi ndi zonse zimene zili mmenemo ndi za Yehova.”*+
14 Taonani, kumwamba ndi kwa Yehova Mulungu wanu, ngakhale kumwamba kwa kumwambako* komanso dziko lapansi ndi zonse zili mmenemo zonsezo ndi zake.+
24 Dziko lapansi ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndi za Yehova,+Nthaka komanso onse okhala panthakapo ndi ake.
12 Ngakhale nditakhala ndi njala, sindingakuuzeni,Chifukwa dziko lonse ndiponso zonse zimene zili mmenemo ndi zanga.+