Salimo 140:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anthu onyada anditchera msampha.Iwo agwiritsa ntchito zingwe kuti atchere ukonde mʼmphepete mwa njira,+ Ndipo anditchera makhwekhwe.+ (Selah)
5 Anthu onyada anditchera msampha.Iwo agwiritsa ntchito zingwe kuti atchere ukonde mʼmphepete mwa njira,+ Ndipo anditchera makhwekhwe.+ (Selah)