Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 9:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Iye adzaweruza anthu okhala padziko lapansi mwachilungamo.+

      Adzapereka zigamulo zolungama pa milandu ya mitundu ya anthu.+

  • Salimo 96:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Lengezani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala Mfumu.+

      Dziko lapansi lakhazikika moti silingasunthidwe.*

      Iye adzaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo.”*+

  • Salimo 98:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Pamaso pa Yehova chifukwa iye akubwera kudzaweruza dziko lapansi.

      Adzaweruza anthu okhala padziko lapansi mwachilungamo+

      Ndipo adzaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo.+

  • Aroma 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Koma chifukwa chakuti sukufuna kusintha, ndipo ukusonyeza mtima wosalapa, Mulungu adzakulanga ndithu pa tsiku la mkwiyo wake akamadzaulula chiweruzo chake cholungama.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena