Salimo 67:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mitundu ya anthu isangalale ndi kufuula mokondwera,+Chifukwa inu mudzaweruza anthu mwachilungamo.+ Mudzatsogolera mitundu ya anthu padziko lapansi. (Selah) Salimo 96:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Lengezani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala Mfumu.+ Dziko lapansi lakhazikika moti silingasunthidwe.* Iye adzaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo.”*+ Aroma 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye adzaweruza aliyense mogwirizana ndi zochita zake.+
4 Mitundu ya anthu isangalale ndi kufuula mokondwera,+Chifukwa inu mudzaweruza anthu mwachilungamo.+ Mudzatsogolera mitundu ya anthu padziko lapansi. (Selah)
10 Lengezani pakati pa anthu a mitundu ina kuti: “Yehova wakhala Mfumu.+ Dziko lapansi lakhazikika moti silingasunthidwe.* Iye adzaweruza mitundu ya anthu mwachilungamo.”*+