Salimo 42:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Mofanana ndi mbawala imene imalakalaka mitsinje ya madzi,Inenso* ndikulakalaka inu Mulungu. 2 Mofanana ndi munthu amene akulakalaka madzi, ndikulakalaka* Mulungu, Mulungu wamoyo.+ Ndidzapita liti kukaonekera pamaso pa Mulungu?*+ Salimo 63:1, 2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+ Ine ndikulakalaka inu.*+ Ndalefuka* chifukwa cholakalaka inuMʼdziko louma komanso lopanda madzi, kumene sikumera chilichonse.+ 2 Choncho ndakuonani mʼmalo oyera.Ndaona mphamvu zanu ndi ulemerero wanu.+
42 Mofanana ndi mbawala imene imalakalaka mitsinje ya madzi,Inenso* ndikulakalaka inu Mulungu. 2 Mofanana ndi munthu amene akulakalaka madzi, ndikulakalaka* Mulungu, Mulungu wamoyo.+ Ndidzapita liti kukaonekera pamaso pa Mulungu?*+
63 Inu Mulungu, ndinu Mulungu wanga, ine ndikukufunafunani.+ Ine ndikulakalaka inu.*+ Ndalefuka* chifukwa cholakalaka inuMʼdziko louma komanso lopanda madzi, kumene sikumera chilichonse.+ 2 Choncho ndakuonani mʼmalo oyera.Ndaona mphamvu zanu ndi ulemerero wanu.+