Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 132:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova walumbira kwa Davide.

      Ndithudi sadzalephera kukwaniritsa mawu ake akuti:

      “Ndidzaika pampando wako wachifumu

      Mmodzi wa ana ako.*+

  • Ezekieli 34:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Ndidzazipatsa mʼbusa mmodzi+ amene ndi mtumiki wanga Davide,+ ndipo adzazidyetsa. Iye adzakhala mʼbusa wawo ndipo azidzazidyetsa.+

  • Hoseya 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Kenako Aisiraeli adzabwerera nʼkuyamba kufunafuna Yehova Mulungu wawo+ ndi Davide mfumu yawo.+ Iwo adzabwera kwa Yehova akunjenjemera ndipo adzafunafuna ubwino wake mʼmasiku otsiriza.+

  • Yohane 7:42
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 42 Kodi si paja lemba limanena kuti Khristu adzachokera mwa ana a Davide+ komanso ku Betelehemu,+ mudzi umene Davide ankakhala?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena